Re: [KA-ALUMNI] Re: kutsanzika-just an observation

11 views
Skip to first unread message

DAVIS NJOBVU

unread,
Sep 18, 2008, 6:25:33 AM9/18/08
to ka-a...@googlegroups.com
Mabwana ndi Madona

kodi obale.uyu yalutitsanzikayu ndiyani poti ine ntapenyetsetsa simdaonepo dzina lake pa yadilesi kapena mchikalata chake.pena inu onzanga mulukumbuka kuti poKadame paja tidali ni Counsel?kodi mnyeyu odali mzwungwu pena munthu,mkwazi pena tonde?

Icho ine nufunonena nchoti ni chifukwa cha mkhalidwe yogwilitsa nchito maina yachidamula ngatomewawa mpo yanthu ena yake yalowelela numatitumizila zinthu zopanda pake.mwina yangathe kukhala odawidyidywa poKadame paja ndiye poopuchita manyazi yagwilitsa ntchito maina yabodza ngati amewawa yoti Counsel,pepani ichi nchitsanzo chabe ati.

Tiyesetse abale yanga kugwilitsa ntchito maina yabwino yaja odatipatsa ya gogo yanthu ngati Alinane,Tilinde,Tisalinde,Tsankho,Mthakati,Chosamva,Chidakwa ni ena otero.
Ine langa ndi Developumentisitiikhumba Mnjobvuta mwachidule kwanti Davis Njobvu.

Zikomo

--- On Tue, 9/9/08, Herbert Nkhoma <hnk...@gmail.com> wrote:

> From: Herbert Nkhoma <hnk...@gmail.com>
> Subject: [KA-ALUMNI] Re: kutsanzika
> To: ka-a...@googlegroups.com
> Date: Tuesday, September 9, 2008, 3:18 AM
> I have seen the messages as well. I have changed all the
> settings to members
> only in the last hour. However I did not find these people
> on our members
> list. I will try and investigate what happened and will
> give you guys a
> report of some sort by the end of the week.
> I have also decided that messages from new members will be
> moderated.
>
> With these changes I think we should wait and see. If it
> does not help then
> I will contact Google for their advice and whatever they
> recommend is what
> we will follow.
>
> Herbert
>
> On Tue, Sep 9, 2008 at 11:18 AM,
> <cou...@globemw.net> wrote:
>
> >
> > amayi ndi abambo,
> >
> > ndati ndikuuzeni za kuchoka kwanga mu guluri.
> >
> > ngati pali zina zoti inuyo mukuganiza kuti ine
> ndikufunika kudziwa nawo
> > mutha kundilembera pandekha; koma ndili okayika.
> >
> > pomaliza ndikusiilreni mawu awa:
> >
> > pagulupa pabwera mauthenga awiri,sindidaatsegule
> popeza kuti mitu yawo
> > inandizizwitsa.koma ndinadabwa kuti kodi atumizawa
> adalowa liti paguluri?
> >
> > kapena adalowa titakamba kale nkhani ija? kapena anali
> atalowa kale?
> > kapena mwina siali muguluri, wangotumiza mwa ukatswiri
> wake? kapenso mwina
> > ndi m'modzi mwa ife?
> >
> > kodi ife ngati gulu talephera kudziteteza? kapena
> talephera kuchita icho
> > chomwe tidagwirizana?
> >
> > kodi ndizotheka kuti amene ali ndi ukatswiri wa
> zoyankhulana munjira
> > yamakono atha kutiuza kumene mauthenga akuchokera?
> >
> > ndidikira mpaka lachinayi kuti ndimve maganizo anu.
> >
> > zikomo.
> >
> >
> >
> >
> >
> > >
> >
>
>
> --
> Herbert Nkhoma
> Cell: +2658866150
>
>



cou...@globemw.net

unread,
Sep 18, 2008, 8:41:39 AM9/18/08
to ka-a...@googlegroups.com
uyu adazelezeka kale kale uyu

DAVIS NJOBVU

unread,
Sep 18, 2008, 10:54:35 AM9/18/08
to ka-a...@googlegroups.com
Oh oh

Uja adatsanzika uja yadakalipo eti?ah munthu wanji otere? O Mawerenga muli bwino? komatu kunena mosabisa gulu ili la KA Aluminium mlozizira zedi.Vuto nchiani ko? kodi ndiye kuti onthu onzeru omankhala a ndwii?pepani langa mfuso?

Counsel chonde titumizileni chinthunzi koma mutavala zovala ati?chifukwa Malawi alunidabwitsa.chikhala mnjale nkadanti nchingozi.kwapenya wena pachithunzi ali dele kunisekelera koma ine chosecho sinuwadziwa!choncho

Alipo amene sodamuone Robert Daison pa shoprite?kodi palibe njira yoti tingathandizile anthu ngati Rob Dai?

Zikomo


--- On Thu, 9/18/08, cou...@globemw.net <cou...@globemw.net> wrote:

cou...@globemw.net

unread,
Sep 22, 2008, 8:28:25 AM9/22/08
to ka-a...@googlegroups.com
PA NKHANI YOTSANZIKA


adatsanzika ndiye adakalipo?

kodi inuyo simudamveko za "suicide note"? munthu amatha kuilemba,
ndikupeza chingwe, koma asadadziponye zimatheka anthu ena kumudulapo
pachingwepo.

zimathanso kutheka kuti amamwa mankwala opanda mphamvu, ndiye timakamuona
kuchipatala, suicide note ija nthawi imeneyo ili ndi apolisi, kapena a
DPP.

ndiye mukawerenganso kalata ndidalemba ija... ndidati depending on the
circumstances ndisamukapo lachinayi

koma inu mudazelezeka! is this the same man who( not that!!!!!!)got 100%
in some greek exam? somewhere in form 3 or 4? I was like mdala uyu waonjeza,
kusowa chochita chani? osangoyamba golf bwanji?


GULULI NDI LOZIZIRA?

pankhani imeneyi i propose that you join another group viz
kamuzu_academy@yahoogroups. In fact, having just walked out of a "mergers
and acquisitions" exercise, I propose that the two groups merely merge.

In that group, my friend, you will be reunited with bra James H Peres as
he unrelentingly bashes the IMF, the World Bank.

bra James seems to like the writings of Chomsky ( www.chomsky.info as a
starting point)


CHITHUNZI

I should send what? you haven't "turned", have you?

I hear an organisation was launched recently. Since we are encouraged to
be tolerant of divergent views and preferences, let me stop here, even
though I have always wondered, is it to do with DNA, genes or is merely
"mental"? does it exist in other animals? Maybe Joel will tell us.

But no photos, did I tell you I got dreadlocks?!!
FINALLY HA HA HA ( but you may go to www.wandawandas.com)


ON AVEC NUTS

some three years ago I chanced upon Rob Dai. I asked him what had gone
down. he said "ife anthu agule mumadziwa ndi opepetulidwa".

i did not believe this, but whatever the case my view is that the solution
( at least one)lies with Rob Dai ...( "but first i know it starts with
me...." )

So if we got any inspirational ( motivational) speakers here, please sit
the man down , it may take a long time, but faith has been known? to move
(or said to be capable of moving) mountains

am out


Joe Nkhoma

unread,
Oct 23, 2008, 11:09:57 AM10/23/08
to ka-a...@googlegroups.com
Good people,

it was sad to hear that Festino is no more. koma alipo anapita to see him
off ? Duncain's article was touching. fare thee well Chims and RIP

Joe

Lovemore Ngoma

unread,
Oct 24, 2008, 3:13:49 AM10/24/08
to ka-a...@googlegroups.com
I pity for his family left behind. My condolences too.

Lovemore

Reply all
Reply to author
Forward
0 new messages