ndati ndikuuzeni za kuchoka kwanga mu guluri.
ngati pali zina zoti inuyo mukuganiza kuti ine ndikufunika kudziwa nawo
mutha kundilembera pandekha; koma ndili okayika.
pomaliza ndikusiilreni mawu awa:
pagulupa pabwera mauthenga awiri,sindidaatsegule popeza kuti mitu yawo
inandizizwitsa.koma ndinadabwa kuti kodi atumizawa adalowa liti paguluri?
kapena adalowa titakamba kale nkhani ija? kapena anali atalowa kale?
kapena mwina siali muguluri, wangotumiza mwa ukatswiri wake? kapenso mwina
ndi m'modzi mwa ife?
kodi ife ngati gulu talephera kudziteteza? kapena talephera kuchita icho
chomwe tidagwirizana?
kodi ndizotheka kuti amene ali ndi ukatswiri wa zoyankhulana munjira
yamakono atha kutiuza kumene mauthenga akuchokera?
ndidikira mpaka lachinayi kuti ndimve maganizo anu.
zikomo.
i was surprised by the messages nane koma tiye tisasiye. i was about to ask
kuti kodi gululi likuloleza pseudonames? chifukwa sizidayenele kutelo and
dzinalija ife likutudabwitsa. anzathu mwazama ndi nkhani za it tithandizeni
Joe